Mbiri Yateokrase
New Zealand: Lipoti la August likusonyeza chiŵerengero chatsopano chapamwamba cha ofalitsa 12,867.
Thailand: Chaka chautumiki cha 1994 chinatha ndi chiŵerengero chatsopano chapamwamba cha ofalitsa 1,487. Chimenechi chinali chiwonjezeko cha 11 peresenti kuposa avareji ya chaka chatha.
Trinidad: Chiŵerengero chapamwamba cha ofalitsa 6,601 chinafikiridwa mu August.