Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsamba 7
  • Esitere Anapulumutsa Anthu a Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Esitere Anapulumutsa Anthu a Mulungu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Anachita Zinthu Mwanzeru, Molimba Mtima Ndiponso Moganizira Ena
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Anachita Zinthu Mwanzeru, Molimba Mtima Ndiponso Moganizira Ena
    Nsanja ya Olonda—2012
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 February tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | ESITERE 1-5

Esitere Anapulumutsa Anthu a Mulungu

Esitere anasonyeza chikhulupiriro komanso kulimba mtima poteteza anthu a Mulungu

  • Esitere akanatha kuphedwa chifukwa chopita kwa mfumu popanda kuitanidwa. Iye anali atatha masiku 30 osaitanidwa ndi mfumu

  • Mfumu Ahasiwero amene ankadziwikanso ndi dzina lakuti Sasta I, anali munthu wankhanza. Panthawi ina anatenga munthu n’kumudula pakati kuti likhale chenjezo kwa anthu ena. Komanso anachotsa Mfumukazi Vasiti pa udindo chifukwa choti sanamvere

  • Esitere anafunika kuulula kuti anali Myuda ndiponso kuuza Mfumu Ahasiwero kuti yapusitsidwa ndi munthu amene inkamudalira

Mfumukazi Esitere akugwira ndodo yachifumu imene mfumu Ahasiwero akumuloza nayo
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena