Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsamba 8
  • Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • “Ufumu Wanu Udze”​​​—Pemphero Limene Anthu Ambiri Amalikonda
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Muzichita Zinthu Monga Nzika za Ufumu
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Kodi Ufumu wa Mulungu Uli Mumtima Mwanu?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 June tsamba 8

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe

A Mboni za Yehova amagwiritsa ntchito makadi poitanira anthu kuti akamvetsere nkhani ya M’baibulo

Anthu omwe akufuna kukhala nzika za Ufumu wa Mulungu ayenera kuyesetsa kuphunzira zokhudza Ufumuwu ndiponso zimene wachita kale panopo. N’chifukwa chiyani ayenera kuchita zimenezi? N’chifukwa chakuti chikhulupiriro chawo chidzakhala cholimba podziwa kuti Ufumu wa Mulungu ukulamulira komanso zimenezi zidzawathandiza kuti aziuza ena uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Sal. 48:12, 13) Mukamaonera vidiyo yakuti Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe, mupeze mayankho a mafunso awa:

  1. N’chifukwa chiyani tinganene kuti “Sewero la Pakanema la Chilengedwe” linathandiza anthu omwe analionera?

  2. Kodi ankagwiritsa ntchito bwanji wailesi pouza anthu uthenga wabwino?

  3. Kodi ndi njira zina ziti zomwe anagwiritsa ntchito pouza anthu uthenga wabwino, nanga zotsatira zake zinali zotani?

  4. Kodi ntchito yophunzitsa anthu utumiki yasintha bwanji m’zaka zapitazi?

  5. Kodi ndi mfundo zothandiza ziti zomwe ophunzira a Sukulu ya Giliyadi anaphunzitsidwa?

  6. Kodi misonkhano ikuluikulu yathandiza bwanji kuphunzitsa anthu a Yehova?

  7. Kodi n’chiyani chimene chimakutsimikizirani kuti Ufumu wa Mulungu ukulamulira?

  8. Kodi timasonyeza bwanji kuti tili kumbali ya Ufumu wa Mulungu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena