June Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda Ya June 2016 Zitsanzo za Ulaliki June 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 34-37 Khulupirira Yehova Ndipo Chita Zabwino MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kugwiritsa Ntchito Mavidiyo Pophunzitsa June 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 38-44 Yehova Amasamalira Anthu Omwe Akudwala June 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 45-51 Yehova Sadzasiya Anthu Amtima Wosweka MOYO WATHU WACHIKHRISTU Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka 100 Ndipo Ukulamulirabe June 27–July 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 52-59 “Umutulire Yehova Nkhawa Zako” MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”