Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsamba 2
  • Tizikhala Moyo Wosalira Zambiri Kuti Titumikire Bwino Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizikhala Moyo Wosalira Zambiri Kuti Titumikire Bwino Mulungu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Diso Lanu Limalunjika Pachinthu Chimodzi?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
  • Khalani ndi Diso la Kumodzi
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2004
  • Khalani ndi Moyo Wolinganizika, Wopepuka
    Nsanja ya Olonda—1989
  • Muzifunafuna Ufumu Osati Zinthu Zina
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 July tsamba 2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Tizikhala Moyo Wosalira Zambiri Kuti Titumikire Bwino Mulungu

Masiku ano pali zinthu zambiri zomwe zingatilepheretse kuchita zinthu zofunika. Mwachitsanzo, pamafunika nthawi komanso mphamvu kuti munthu apite kukagula zinthu, alipire zimene wagula, akonzetse komanso kuteteza zinthuzo kuti ena asamubere. Yesu ankakhala moyo wosalira zambiri chifukwa sankafuna kuti zinthu zina zimulepheretse kuchita utumiki wake.​—Mat. 8:20.

Banja lili kumisonkhano ya Mboni za Yehova

Kodi ndi zinthu ziti zimene mukufuna kusintha pa moyo wanu kuti muzichita zambiri mu utumiki? Kodi mungasinthe zinthu zina ndi zina kuti munthu wina wa m’banja lanu ayambe upainiya? Ngati panopa mumachita kale utumiki wa nthawi zonse, kodi mwayamba kulola kuti zinthu zina zikulepheretseni kuchita zinthu zofunika kwambiri? Munthu amene amatumikira Yehova amasangalala kwambiri ngati amakhala moyo wosalira zambiri.​—1 Tim. 6:7-9.

Lembani zimene mungachite kuti muzikhala moyo wosalira zambiri.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena