CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 142-150
“Yehova ndi Wamkulu ndi Woyenera Kutamandidwa Kwambiri”
Davide anaona kuti ukulu wa Yehova ndi wosasanthulika ndipo zimenezi zinachititsa kuti azitamanda Yehova
Mofanana ndi Davide, atumiki a Yehova okhulupirika amayesetsa kuuza ena ntchito zodabwitsa za Yehova
Davide ankakhulupirira kuti Yehova amafunitsitsa kuthandiza atumiki ake