Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsamba 8
  • Munthu Akamagwiritsa Ntchito Udindo Wake Molakwika Amachotsedwa pa Udindowo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Munthu Akamagwiritsa Ntchito Udindo Wake Molakwika Amachotsedwa pa Udindowo
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Mulungu Amatilangiza Chifukwa Chotikonda
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Kodi Nchiyani Chiyenera Kuchitidwa Minisitala Atachimwa?
    Galamukani!—1992
  • Kodi Mukudziwa?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Mfundo Zazikulu za M’buku la Yesaya—Gawo 2
    Nsanja ya Olonda—2007
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 December tsamba 8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 17-23

Munthu Akamagwiritsa Ntchito Udindo Wake Molakwika Amachotsedwa pa Udindowo

Sebina anali “kapitawo woyang’anira nyumba ya mfumu,” ndipo n’kutheka kuti inali nyumba ya Mfumu Hezekiya. Pa udindo umenewu, iye anali wachiwiri kwa mfumu ndipo ankayenera kuthandiza Aisiraeli.

Sebina akulamula anthu kugwira ntchito pa manda ake

22:15, 16

  • Sebina ankayenera kusamalira zimene anthu a Yehova ankafunikira

  • Iye anasonyeza kudzikonda chifukwa anachita zinthu zongofuna kuti atchuke

22:20-22

  • Yehova anachotsa Sebina pa udindo wake n’kuikapo Eliyakimu

  • Eliyakimu anapatsidwa “makiyi a nyumba ya Davide,” zomwe zikuimira mphamvu komanso ulamuliro

Taganizirani izi: Kodi Sebina akanagwiritsa ntchito bwanji udindo wake kuti athandize anthu ena?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena