Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 May tsamba 6
  • Leka ‘Kufunafuna Zinthu Zazikulu’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Leka ‘Kufunafuna Zinthu Zazikulu’
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Baruki Mlembi Wokhulupirika wa Yeremiya
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Pewani ‘Kufunafuna Zinthu Zazikulu’
    Zimene Mulungu Akutiuza Kudzera mwa Yeremiya
  • Pezani Anzanu Apamtima Mapeto Asanafike
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • “Ine Ndili ndi Iwe Kuti Ndikulanditse”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 May tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 44-48

Leka ‘Kufunafuna Zinthu Zazikulu’

45:2-5

Zikuoneka kuti Baruki anali munthu wophunzira kwambiri ndipo ankagwira ntchito m’nyumba ya mfumu. Ngakhale kuti ankalambira Yehova komanso ankathandiza Yeremiya mokhulupirika, nthawi ina anachita zinthu mosaganiza bwino. Iye anayamba ‘kufunafuna zinthu zazikulu,’ mwina ankafuna kutchuka kapena chuma. Choncho anafunika kusintha maganizo kuti apulumuke pamene Yerusalemu ankawonongedwa.

Pamene Baruki ankatumikira ngati mlembi wa Yeremiya, ankaganizira zokhala ndi chuma chambiri komanso kutchuka
Tchati chosonyeza nthawi imene Yeremiya anayamba ntchito yake ya uneneri, pamene Baruki anayamba kumuthandiza ndiponso pamene Yerusalemu anawonongedwa
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena