CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 18-20
Kodi Yehova Akatikhululukira Machimo, Amawakumbukirabe?
Yehova akatikhululukira machimo, sangadzatiimbenso mlandu pa zolakwazo m’tsogolo.
Zitsanzo za m’Baibulo zotsatirazi zimatithandiza kukhulupirira kuti Yehova amakhululuka.
Mfumu Davide
Kodi ndi zoipa zotani zimene anachita?
Kodi anamukhululukira chifukwa chiyani?
Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti anamukhululukira?
Mfumu Manase
Kodi ndi zoipa zotani zimene anachita?
Kodi anamukhululukira chifukwa chiyani?
Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti anamukhululukira?
Mtumwi Petulo
Kodi ndi zoipa zotani zimene anachita?
Kodi anamukhululukira chifukwa chiyani?
Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti anamukhululukira?