Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp20 No. 3 tsamba 16
  • Kodi Munayamba Mwadzifunsapo Kuti:

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Munayamba Mwadzifunsapo Kuti:
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?
    Kodi Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo Tingawapeze Kuti?
  • Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?
    Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?
  • Kodi Baibulo Mumalikhulupirira?
    Kodi Baibulo Mumalikhulupirira?
  • Kodi N’chiyani Chingathandize Kuti Banja Likhale Losangalala?
    Kodi N’chiyani Chingathandize Kuti Banja Likhale Losangalala?
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
wp20 No. 3 tsamba 16

Kodi Munayamba Mwadzifunsapo Kuti:

  • Patebulo pali foni komanso makapu awiri a khofi. Kabuku kakuti ‘Real Faith​​—Your Key to a Happy Life’ kakuoneka pafoniyo.

    N’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri chonchi?

  • Kodi mungapeze kuti nzeru zokuthandizani kulimbana ndi mavuto?

  • Kodi Mulungu amasamala za inuyo panokha?​—1 Petulo 5:6, 7.

  • Kodi mungadziwe bwanji zokhudza Mulungu ndi zimene amafuna?

Anthu mamiliyoni ambiri apeza mayankho othandiza a mafunso amenewa pophunzira Malemba Opatulika. Nanunso mukhoza kupeza mayankho a mafunsowa.

Ngati mukufuna kumva zambiri, pemphani amene amafalitsa magaziniyi kuti akupatseni kwaulere kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu kapenanso werengani kabukuka pa www.jw.org.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena