CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 23-24
Muzikhala Okonzeka Kukhululuka
Kodi ndi ndani amene ndingafunike kumukhululukira?
Kodi kukhala “wokonzeka kukhululuka” kumatanthauza chiyani? (Sal. 86:5) Yehova ndi Mwana wake amaona mmene mtima wa munthu ulili kuti aone ngati wasintha n’cholinga choti amukhululukire.