Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsamba 6
  • “Simuli Mbali ya Dzikoli”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Simuli Mbali ya Dzikoli”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Khalani Olimba Mtima!
    Nsanja ya Olonda—1993
  • ‘Limba Mtima Ndipo Ugwire Ntchitoyi’
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • “Taona! Mkango wa Fuko la Yuda”
    ‘Bwera Ukhale Wotsatira Wanga’
  • Khalani Omvera Ndiponso Olimba Mtima Ngati Khristu
    Nsanja ya Olonda—2009
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 October tsamba 6
Yesu akulankhula ndi atumwi ake okhulupirika

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 15-17

“Simuli Mbali ya Dzikoli”

15:19, 21; 16:33

  • Yesu anagonjetsa dziko popewa kuchita zinthu za m’dzikoli

  • Otsatira a Yesu amayenera kuchita zinthu molimba mtima kuti asasokonezeke ndi maganizo komanso zochita za anthu a m’dzikoli

  • Kutengera chitsanzo cha Yesu yemwe anagonjetsa dziko kungatithandize kuti tizichita zinthu molimba mtima

Kodi ndi zinthu ziti zimene zingachititse kuti ndikhale mbali ya dzikoli?

Kodi ndi zinthu ziti zomwe zimafalitsidwa pa TV, m’manyuzipepala kapena pa intaneti zimene zingachititse kuti ndikhale mbali ya dzikoli?

M’bale wachichepere sakuimba nawo nyimbo yafuko; m’bale akukana ntchito inayake; m’bale akulalikira anzake; m’bale ndi mkazi wake akulankhulana ndi dokotala
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena