Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsamba 6
  • October 22-28

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 22-28
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 October tsamba 6

October 22-28

YOHANE 15-17

  • Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Simuli Mbali ya Dzikoli”: (10 min.)

    • Yoh. 15:19​—Otsatira a Yesu ‘sali mbali ya dzikoli’ (“dziko” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 15:19, nwtsty)

    • Yoh. 15:21​—Anthu amadana ndi otsatira a Yesu chifukwa cha dzina lake (“chifukwa cha dzina langa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 15:21, nwtsty)

    • Yoh. 16:33​—Otsatira a Yesu angathe kugonjetsa dziko ngati atamayesetsa kumutsanzira (it-1 516)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 17:21-23​—Kodi otsatira a Yesu amakhala “amodzi” m’njira yotani? (“amodzi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 17:21, nwtsty; “akhale mu umodzi weniweni” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 17:23, nwtsty)

    • Yoh. 17:24​—Kodi mawu akuti “musanayale maziko a dziko” akutanthauza chiyani? (“musanayale maziko a dziko” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 17:24, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 17:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 14 ¶3-4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 101

  • “Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Chikondi—Muziteteza Mgwirizano Wathu Wamtengo Wapatali”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti ‘Muzikondana’​—Musamasunge Zifukwa. Ngati nthawi ilipo, kambiranani mfundo za m’kabokosi kakuti “Chitsanzo cha M’Baibulo Chofunika Kuchiganizira.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 10, ndi bokosi lakuti “Ulendo Wosangalatsa”

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena