Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsamba 4
  • “Uike Akulu”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Uike Akulu”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Oyang’anira ndi Atumiki Otumikira Amaikidwa Mwateokalase
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Kodi Mpingo wa Chikhristu Umayendetsedwa bwanji?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Oyang’anira Amene Amaweta Nkhosa za Mulungu
    Gulu Lochita Chifuniro cha Mulungu
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 August tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | TITO 1–FILIMONI

“Uike Akulu”

Tito 1:5-9

Tito akukambirana ndi abale

Paulo anauza Tito kuti ‘aike akulu mumzinda uliwonse.’ Zimenezi ndi zomwenso oyang’anira madera amachita akamaika akulu m’mipingo.

BUNGWE LOLAMULIRA

Potsatira zimene zinkachitika m’nthawi ya atumwi, Bungwe Lolamulira linapereka udindo wofunika kwambiri kwa oyang’anira madera woti aziika akulu komanso atumiki othandiza.

Mabokosi okonzedwa ngati mivi osonyeza mmene zinthu zimayendera

OYANG’ANIRA MADERA

Woyang’anira dera aliyense ayenera kuchita zinthu mosamala kwambiri komanso kupemphera asanaike munthu amene akulu amuvomereza kuti akhale paudindo.

Mabokosi okonzedwa ngati mivi osonyeza mmene zinthu zimayendera

AKULU

Ngakhale munthu ataikidwa paudindo, ayenera kupitirizabe kukwaniritsa ziyeneretso za m’Malemba.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena