Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsamba 4
  • August 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 12-18
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 August tsamba 4

August 12-18

TITO 1–FILIMONI

  • Nyimbo Na. 99 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Uike Akulu”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Tito.]

    • Tito 1:5-9​—Oyang’anira madera amaika abale omwe akwaniritsa ziyeneretso za m’Malemba kuti akhale akulu (w14 11/15 28-29)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Filimoni.]

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Tito 1:12​—N’chifukwa chiyani tinganene kuti lembali silikulimbikitsa tsankho? (w89 5/15 31 ¶5)

    • Filim. 15, 16​—N’chifukwa chiyani Paulo sanapemphe Filimoni kuti amasule Onesimo? (w08 10/15 31 ¶5)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Tito 3:1-15 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 3)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 84

  • “Achinyamata, Mukhale ‘Odzipereka pa Ntchito Zabwino’”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Achinyamata Amene Akulemekeza Yehova.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 46

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena