Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 October tsamba 2
  • Muzisonyeza Nzeru Yochokera kwa Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzisonyeza Nzeru Yochokera kwa Mulungu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mumagwiritsa Ntchito “Nzeru Yochokera Kumwamba” pa Moyo Wanu?
    Yandikirani Yehova
  • “Kodi Wanzeru ndi Womvetsa Zinthu Ndani Pakati pa Inu?”
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Pulogalamu Yatsopano ya Msonkhano Wadera
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
  • ‘Wodala Munthu Wopeza Nzeru’
    Nsanja ya Olonda—2001
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 October tsamba 2
Mlongo akusinkhasinkha zimene wawerenga m’Baibulo, akuganizira nthawi imene anakangana ndi mlongo wina ndipo wapita kukakambirana naye

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YAKOBO 3-5

Muzisonyeza Nzeru Yochokera kwa Mulungu

3:17

Nzeru yochokera kwa Yehova ndi yothandiza kwambiri. Mwachitsanzo, ingatithandize kuti tiyambirenso kugwirizana ndi Akhristu anzathu. Zomwe timachita zimasonyeza ngati tikugwiritsa ntchito nzeru yochokera kwa Mulungu kapena ayi.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi chaposachedwapa ndasonyeza makhalidwe ati mwa makhalidwe ali m’munsiwa? Kodi ndiyenera kuchita zotani kuti ndizitha kusonyeza makhalidwewa?’

  • Woyera

  • Wamtendere

  • Wololera

  • Wokonzeka kumvera

  • Wodzaza ndi chifundo ndiponso zipatso zabwino

  • Wopanda tsankho

  • Wopanda chinyengo

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena