Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 6
  • “Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • “Zinthu Zakale Sizidzakumbukiridwanso”
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Dziko Latsopano Limene Mulungu Walonjeza
    Dikirani!
  • Dziko Latsopano Lopanda Mavuto
    Galamukani!—1990
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 6
Yerusalemu watsopano wamaziko a miyala ya yasipi womwe mzinda wake uli mkati mwa galasi

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 20-22

“Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”

21:1-5

Yehova akulonjeza kuti adzapanga zinthu zonse kukhala zatsopano.

  • “Kumwamba kwatsopano”: Boma latsopano limene lidzakhazikitse chilungamo padziko lapansi

  • “Dziko lapansi latsopano”: Anthu amene amamvera ulamuliro wa Mulungu komanso kutsatira mfundo zake zolungama

  • “Zinthu zonse . . . n’zatsopano”: Tsiku lililonse tizidzakhala ndi zinthu zotichititsa kukhala osangalala ndipo tidzaiwaliratu mavuto onse amene tikukumana nawo panopa

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena