Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 April tsamba 5
  • Kodi Mukuyesetsa Kuchita Zonse Zomwe Mungathe Kuti Mupeze Madalitso?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mukuyesetsa Kuchita Zonse Zomwe Mungathe Kuti Mupeze Madalitso?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Muzifunafuna Madalitso a Yehova ndi Mtima Wonse
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Kodi Yehova Amalidalitsa Liti Khama la Munthu?
    Nsanja ya Olonda—2002
  • Pitirizani Kulimbana ndi Zimene Zingakulepheretseni Kupeza Madalitso
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda—2007
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 April tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 32-33

Kodi Mukuyesetsa Kuchita Zonse Zomwe Mungathe Kuti Mupeze Madalitso?

32:24-28

Kuti Yehova atidalitse, tiyenera kuchita khama kwambiri komanso kuonetsetsa kuti kutumikira Yehova kuzikhala pamalo oyamba pamoyo wathu. (1Ak 9:26, 27) Ngakhale kuti Yakobo anali wachikulire, anasonyeza khama ndipo nafenso tiyenera kutengera chitsanzo chake. Tingasonyeze kuti timafunitsitsa kuti Yehova atidalitse . . .

  • Tikamakonzekera bwino misonkhano yampingo

  • Tikamalalikira nthawi zonse

  • Tikamayesetsa kuthandiza ena mumpingo

Mayi wachitsikana yemwe amakhala wotanganidwa. Chithunzi choyamba: Akupemphera asanayambe zochitika za tsikulo. Chachiwiri: Akudyetsa mwana wake asanapite muutumiki. Chachitatu: Akulalikira mosangalala ndi ana ake awiri komanso alongo a mumpingo wake.

Kaya tikukumana ndi mavuto otani, tiyenera kumapemphera kwa Yehova nthawi zonse kuti atithandize komanso kumamutumikira ndi mtima wonse kuti atidalitse.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi zinthu ziti zomwe ndikufunika kuyesetsa kumazichita mwakhama kuti Yehova azindidalitsa?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena