Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 June tsamba 2
  • Yosefe Anakhululukira Azichimwene Ake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yosefe Anakhululukira Azichimwene Ake
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Muzikhala Okonzeka Kukhululuka
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Kukhululukira ndi Kuiŵala—Kodi Nkotheka Motani?
    Galamukani!—1995
  • “Kodi Ine Ndatenga Malo a Mulungu?”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • ‘Pitirizani Kukhululukirana Eni Okha’
    Nsanja ya Olonda—1997
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 June tsamba 2
Yosefe akudziulula kwa azichimwene ake, ndipo iwo akudabwa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 44-45

Yosefe Anakhululukira Azichimwene Ake

44:1, 2, 33, 34; 45:4, 5

Kukhululuka kumakhala kovuta makamaka ngati munthu watikhumudwitsa mwadala. Kodi n’chiyani chinathandiza Yosefe kukhululukira azichimwene ake atamulakwira?

  • Yosefe sanabwezere azichimwene ake koma anawakhululukira ataona kuti asintha.​—Sal. 86:5; Luka 17:3, 4

  • Iye sanawasungire chakukhosi koma m’malomwake anatsanzira Yehova amene amakhululuka ndi mtima wonse.​—Mika 7:18, 19

Kodi ndingatsanzire bwanji Yehova pa nkhani yokhululuka?

Zithunzi: 1. Alongo awiri akucheza ku Nyumba ya Ufumu. 2. Abale awiri akupatsana moni.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena