Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 October tsamba 6
  • Anathandizidwa Kugwira Ntchito ya Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anathandizidwa Kugwira Ntchito ya Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mungadandaule Ngati Anthu Saona Ntchito Yanu?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Anthu Okhulupirika Akale Amene Anatsogoleredwa ndi Mzimu wa Mulungu
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Mphatso ya Yehova ya Mzimu Woyera
    Nsanja ya Olonda—1992
  • Mzimu wa Mulungu Unkatsogolera Akhristu Oyambirira Ndipo Ukutsogoleranso Akhristu Masiku Ano
    Nsanja ya Olonda—2011
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 October tsamba 6
Bezaleli ndi Oholiabu akupanga zinthu zagolide zoti zikhale m’chihema. Mmodzi akugwiritsa ntchito nyundo popanga phiko la kerubi pomwe winayo akusalaza golide ndi nyundo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 35-36

Anathandizidwa Kugwira Ntchito ya Yehova

35:25, 26, 30-35; 36:1, 2

Mzimu woyera wa Yehova unathandiza Bezaleli ndi Oholiabu kuti apange chihema mogwirizana ndi mapulani ake. (Onani chithunzi chapachikuto.) Mzimu woyera wa Yehova ungathandizenso atumiki ake masiku ano. Kodi tingatani kuti uzitithandiza?

  • Tiyenera kupempha kuti mzimu woyera uzitithandiza kuwonjezera luso lathu potumikira Yehova

  • Tiyenera kumaphunzira Mawu a Mulungu mwakhama

  • Tiyenera kuchita ndi mtima wonse utumiki uliwonse umene tapatsidwa

A Mboni za Yehova akuchita utumiki wosiyanasiyana. 1. Alongo akugwira ntchito yomanga. 2. M’bale akukonzekera kukachititsa Phunziro la ‘Nsanja ya Olonda.’ 3. M’bale akulalikira mwini shopu pamene mnzake akuyang’ana kuona ngati anthu otsutsa akubwera. 4. Banja lili ku Sukulu ya Olalikira za Ufumu.

Kodi Yehova angakuthandizeni kugwira ntchito ziti?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena