Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 October tsamba 7
  • October 26–November 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 26–November 1
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 October tsamba 7

October 26–November 1

EKISODO 37-38

  • Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Maguwa Ansembe a Chihema Anali Ofunika pa Kulambira Koona”: (10 min.)

    • Eks 37:25​—Guwa lansembe zofukiza linali m’Malo Oyera (it-1 82 ¶3)

    • Eks 37:29​—Zofukiza zinkasakanizidwa mwaluso kwambiri (it-1 1195)

    • Eks 38:1​—Guwa lansembe zopsereza linali m’bwalo la chihema (it-1 82 ¶1)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Eks 37:1, 10, 25​—N’chifukwa chiyani mtengo wa mthethe unali wabwino kupangira chihema? (it-1 36)

    • Eks 38:8​—Kodi magalasi odziyang’anira akale ankasiyana bwanji ndi amasiku ano? (w15 4/1 15 ¶4)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 37:1-24 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako gawirani magazini yaposachedwapa imene ili ndi nkhani yomwe mwininyumba anayambitsa. (th phunziro 12)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 199 ¶8-9 (th phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 67

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • “Tidzagwira Ntchito Yapadera mu November Yolengeza za Ufumu wa Mulungu”: (10 min.) Nkhani Yokambirana. Onerani ndi kukambirana vidiyo ya ulendo woyamba ya November.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 106

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 16 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena