Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 October tsamba 7
  • Maguwa Ansembe a Chihema Anali Ofunika pa Kulambira Koona

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Maguwa Ansembe a Chihema Anali Ofunika pa Kulambira Koona
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo Limakukhudzani Bwanji?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Kufukiza Kodi N’kofunika pa Kulambira Koona?
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Kodi Guwa la Nsembe N’lofunika Polambira?
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Kodi Mapemphero Anu ‘Amakonzedwa Ngati Chofukiza’?
    Nsanja ya Olonda—1999
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 October tsamba 7
Chithunzi chosonyeza chihema komanso mmene mkati mwake munkaonekera, nsalu zake zotchinga zapindidwa ndipo mkatimo mukuonekera. Pafupi ndi chihemachi pali beseni losambira lamkuwa komanso guwa la nsembe zopsereza

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 37-38

Maguwa Ansembe a Chihema Anali Ofunika pa Kulambira Koona

37:25, 29; 38:1

Maguwa ansembe a chihema anapangidwa potsatira malangizo a Yehova ndipo ankaimira zinthu zapadera.

  • Guwa lansembe zofukiza.

    Mofanana ndi kupereka zofukiza zosakanizidwa mwaluso, mapemphero ovomerezeka amene atumiki a Yehovafe timapereka kwa iye amamusangalatsa

  • Guwa la nsembe zopsereza.

    Yehova ankalandira nsembe zimene zinkaperekedwa paguwa lansembe zopsereza. Guwali linali patsogolo pa malo opatulika m’bwalo la chihema ndipo zimenezi zimatikumbutsa kuti tiyenera kukhulupirira nsembe ya dipo ya Yesu kuti tisangalatse Mulungu.​—Yoh 3:16-18; Ahe 10:5-10

Kodi tingakonzekere bwanji mapemphero athu kuti akhale ngati zofukiza kwa Mulungu?—Sl 141:2

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena