Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 4
  • Yehova Amafuna Kuti Anthu Ake Azikhala Osiyana ndi Ena

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Amafuna Kuti Anthu Ake Azikhala Osiyana ndi Ena
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mungatani Kuti Yehova Azikudalitsani?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Anachita Zinthu Mwanzeru Pogawa Malo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muziteteza Cholowa Chanu Chomwe Ndi Chamtengo Wapatali
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amafuna Kuti Anthu Ake Azikhala Osiyana ndi Ena

Tiyenera kumvera malamulo onse a Yehova (Le 20:​22, 23; w04 10/15 11 ¶12)

Yehova amalonjeza kuti adzapereka cholowa (Le 20:24; it-1 1199)

Yehova amafuna kuti kulambira kwa anthu ake kuzikhala koyera (Le 20:​25, 26; it-1 317 ¶2)

Yehova amadalitsa anthu amene amakhalabe naye pa ubwenzi wolimba. Kuti apitirize kusangalala nafe, tiyenera kukhala osiyana ndi anthu a m’dzikoli komanso kupewa makhalidwe oipa.

M’bale wa m’Komiti Yolankhulana ndi Achipatala akupereka kwa dokotala mapepala a malangizo omwe angatsatire pothandiza odwala a Mboni.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi thandizo lachipatala liti limene ndiyenera kupewa kuti ndikondweretse Mulungu?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena