Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 12
  • Yehova Amachita Zinthu Mwadongosolo Ndi Anthu Ake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Amachita Zinthu Mwadongosolo Ndi Anthu Ake
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amatsogolera Anthu Ake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Mumaphunzirapo Kanthu Mukalakwitsa Zinazake?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amachita Zinthu Mwadongosolo ndi Anthu Ake

[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Numeri.]

Aisiraeli ankamanga mahema m’magulu a mafuko atatuatatu (Nu 1:​52, 53; w94 12/1 9 ¶4)

Mumsasa wa Aisiraeli muyenera kuti munali anthu 3 miliyoni kapena kuposa (Nu 2:​32, 33; it-1 397 ¶4)

Yehova amafuna kuti anthu ake azimulambira mwadongosolo. Aisiraeli ankalambira Yehova mwadongosolo, ndipo umu ndi mmenenso zilili ndi ife masiku ano.​—1Ak 14:​33, 40.

Mmene msasa wa Aisiraeli unkaonekera kuchokera m’mwamba. Chihema chopatulika chili pakati. Pafupi kwambiri ndi chihema chopatulika pali mabanja a m’fuko la Levi: Aroni kum’mawa, Akohati kum’mwera. Agerisoni kumadzulo ndi Amerari kumpoto. Mafuko 12 a Aisiraeli ali kutali ndi chihema chopatulika. Kum’mawa kuli Isakala, Yuda ndi Zebuloni. Kum’mwera kuli Gadi, Rubeni ndi Simiyoni. Kumadzulo kuli Benjamini, Efuraimu ndi Manase. Kumpoto kuli Nafitali, Dani ndi Aseri.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimagwirizana ndi mtima wonse ndi zimene gulu la Yehova limachita?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena