Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 15
  • Kodi Mungatsanzire Bwanji Anaziri?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungatsanzire Bwanji Anaziri?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Chitani Zochuluka—Monga Anaziri
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Zimene Tingaphunzire kwa Anaziri
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
  • Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Utumiki wa Alevi
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 15

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mungatsanzire Bwanji Anaziri?

Anaziri ankalolera kudzimana zinthu zina (Nu 6:​2-4; it-2 477)

Anaziri ankagonjera n’kumatsatira zofuna za Yehova (Nu 6:5)

Anaziri ankachita zonse zimene Yehova ankafuna kuti akhalebe oyera (Nu 6:​6, 7)

Masiku ano, Akhristu amene ali muutumiki wa nthawi zonse amasonyeza mtima wodzimana ndipo amagonjera Yehova komanso dongosolo lake.

Abale ndi alongo a mu utumiki wa nthawi zonse. 1. Apainiya awiri akulalikira bambo amene ali pabulu. 2. M’bale ndi mlongo akugwira ntchito ya zomangamanga.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena