Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 11
  • Muziyesetsa Kukhalabe Ofatsa Mukapanikizika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muziyesetsa Kukhalabe Ofatsa Mukapanikizika
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Khalanibe Paubwenzi ndi Mulungu Ngakhale Zinthu Zitasintha
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Yesetsani Kukhala Ofatsa Kuti Muzisangalatsa Yehova
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 11
M’bale wachinyamata akupita kumisonkhano. Bambo ake omwe si Mboni apsa mtima ndipo akumukalipira koma iye sakuyankha. M’nyumba muli zokongoletsera zambiri zachipembedzo kuphatikizapo mtengo wa Khirisimasi.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muziyesetsa Kukhalabe Ofatsa Mukapanikizika

Mose, yemwe anali munthu wofatsa, anayesedwa pamene anapanikizika komanso anali ndi nkhawa (Nu 20:2-5; w19.02 12 ¶19)

Pa nthawi ina Mose analephera kukhalabe wofatsa ndipo anapsa mtima (Nu 20:10; w19.02 13 ¶20-21)

Yehova anapereka chilango kwa Mose ndi Aroni chifukwa cha zimene analakwitsa (Nu 20:12; w09 9/1 19 ¶5)

Munthu wofatsa sakwiya msanga komanso sakhala wonyada kapena wodzikuza. Anthu ena akamukhumudwitsa, amakhala woleza mtima, sakwiya, sasunga zifukwa komanso sakhala ndi mtima wofuna kubwezera.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena