Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 8
  • Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mungatani Kuti Mulungu Akhale Mnzanu?
    Zimene Baibulo Limaphunzitsa
  • Yobu Analemekeza Dzina la Yehova
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Sitifunika Kukhala Angwiro Kuti Tikhale Okhulupirika
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Mukulowetsedwa m’Nkhani Yofunika
    Mungathe Kukhala ndi Moyo Kosatha m’Paradaiso pa Dziko Lapansi
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yobu.]

Satana ankanena kuti Yobu ankatumikira komanso kukonda Yehova chifukwa cha dyera (Yob 1:​8-11; w18.02 6 ¶16-17)

Satana amanena kuti ifenso sitikonda Yehova ndi mtima wonse (Yob 2:​4, 5; w19.02 5 ¶10)

Mlongo wavala chipewa chodzitetezera ndipo akulalikira kwa mayi wina pambuyo pa ngozi yam’chilengedwe.

Yehova anapereka mwayi kwa tonsefe woti tizisonyeza kuti Satana ndi wabodza. (Miy 27:11) Tingasonyeze kuti timakonda kwambiri Yehova pochita zinthu zomusangalatsa kaya zinthu zili bwino pa moyo wathu kapena ayi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena