CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Sitifunika Kukhala Angwiro Kuti Tikhale Okhulupirika
Yobu analakwitsa podzudzula Mulungu (Yob 27:1, 2)
Yobu ankadziona kuti ndi wokhulupirika ngakhale kuti ankalakwitsa zinthu zina (Yob 27:5; it-1 1210 ¶4)
Sitifunika kukhala angwiro kuti tikhale okhulupirika, chomwe chimangofunika ndi kukonda Yehova ndi mtima wonse (Mt 22:37; w19.02 3 ¶3-5)
FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi Kudziwa kuti Yehova safuna kuti tizichita zinthu ngati anthu angwiro kumatithandiza bwanji kuti tisafooke?