November Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, November-December 2023 November 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso ndi Moyo?” MOYO WATHU WACHIKHRISTU ‘Muziika Kenakake Pambali’ November 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Musamatsanzire Elifazi Potonthoza Ena November 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Musamasiye Akhristu Anzanu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kulimbikitsa Anthu Omwe Amatumikira pa Beteli November 27–December 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Chuma Sichipangitsa Munthu Kukhala Wolungama MOYO WATHU WACHIKHRISTU ‘Mukhale Okhutira Ndi Zimene Muli Nazo Panopa’ December 4-10 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU ‘Kodi Munthu Angakhale Waphindu kwa Mulungu?’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU Makolo, Muziphunzitsa Ana Anu Kudziwa Mmene Angasangalatsire Mulungu December 11-17 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Sitifunika Kukhala Angwiro Kuti Tikhale Okhulupirika MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kukhulupirika Kumagwirizana ndi Zimene Timaganiza December 18-24 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Muli ndi Mbiri Ngati ya Yobu? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zochita Zanga Zimathandiza Kuti Gulu Lathu Likhale ndi Mbiri Yabwino December 25-31 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Yobu Anachita Kuti Akhalebe Woyera MOYO WATHU WACHIKHRISTU N’chifukwa Chiyani Kuonera Zolaula N’koipa? KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene