Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 3
  • Muzikwaniritsa Zimene Mwalonjeza

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzikwaniritsa Zimene Mwalonjeza
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Tiyenera Kukwaniritsa Zoŵinda Zathu?
    Galamukani!—1993
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2002
  • “Uzikwaniritsa Zinthu Zimene Walonjeza”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Anthu Okhulupirika kwa Yehova Amakwaniritsa Zimene Alonjeza
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzikwaniritsa Zimene Mwalonjeza

Aisiraeli ankalonjeza zinthu mwakufuna kwawo koma ankafunika kukwaniritsa zimene alonjezazo (Nu 30:2; it-2 1162)

Malonjezo ena ankafuna kuti wolonjezayo azipewa zinthu zina ngakhale kuti zinthuzo sizolakwika (Nu 30:3, 4; it-2 1162)

Yehova masiku ano amachita zinthu ndi mtumiki wake aliyense payekha (Nu 30:6-9; w04 8/1 27 ¶3)

Malonjezo awiri ofunika kwambiri amene Mkhristu angapange masiku ano ndi lonjezo lokhudza kudzipereka kwa Mulungu komanso la ukwati.

Anthu akulonjeza. 1. Mtsikana akupemphera. 2. Mwamuna ndi mkazi akuvekana mphete pa ukwati wawo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndikuchita zinthu zonse zomwe ndinalonjeza?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena