Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 16
  • Muzisankha Zinthu Mwanzeru pa Nkhani ya Mowa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzisankha Zinthu Mwanzeru pa Nkhani ya Mowa
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Muli ndi Lingaliro Laumulungu pa Moŵa?
    Nsanja ya Olonda—1996
  • Kodi Kumwa Mowa N’kulakwa?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yokhudza Mowa?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Kodi Banja Lingathandize Motani?
    Galamukani!—1992
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 16

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzisankha Zinthu Mwanzeru pa Nkhani ya Mowa

Chithunzi cha m’vidiyo yakuti ‘Ganizirani Zimene Zingachitike Ngati Mutamwa Mowa.’ Njoka ya mano yatuluka mu tambula ya mowa imene mnyamata wanyamula.

Akhristu onse ayenera kuchita zinthu modziletsa pa nkhani ya mowa. (Miy 23:20, 29-35; 1Ak 6:9, 10) Ngati Mkhristu wasankha kumwa mowa, sayenera kumwa kwambiri. Akuyeneranso kupeweratu kudalira mowa kuti achite zinazake komanso sakuyenera kukhumudwitsa anthu ena. (1Ak 10:23, 24; 1Ti 5:23) Sitikuyenera kukakamiza aliyense kuti amwe mowa, makamaka ana.

ONERANI VIDIYO YAMAKATUNI YAKUTI GANIZIRANI ZIMENE ZINGACHITIKE NGATI MUTAMWA MOWA, NDIPO KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • N’chifukwa chiyani Akhristu onse ayenera kutsatira malamulo a m’dera lawo pa nkhani yomwa mowa?​—Aro 13:1-4

  • N’chifukwa chiyani sitiyenera kulola anthu ena kutikakamiza kuti timwe mowa?​—Aro 6:16

  • Kodi tingapewe bwanji mavuto omwe angabwere chifukwa cha mowa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena