KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Zimene Tinganene
Ulendo Woyamba
Funso: Kodi Mulungu analenga anthu chifukwa chiyani?
Lemba: Ge 1:28
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi timadziwa bwanji kuti cholinga cha Mulungu polenga anthu chidzakwaniritsidwa?
LEMBALI LIKUPEZEKA MU:
Ulendo Wobwereza
Funso: Kodi timadziwa bwanji kuti cholinga cha Mulungu polenga anthu chidzakwaniritsidwa?
Lemba: Yes 55:11
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi moyo udzakhala wotani Mulungu akadzakwaniritsa cholinga chimene analengera anthu?
LEMBALI LIKUPEZEKA MU: