Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 2
  • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambira Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambira Bwanji?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Mfundo Zothandiza Kuweruza Milandu Mwachilungamo
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Akazi?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amaona Kuti Moyo wa Munthu Ndi Wamtengo Wapatali
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambira Bwanji?

Aisiraeli ankafunika kumvera, kukonda komanso kutumikira Yehova ndi mtima wonse komanso moyo wawo wonse (De 11:13; it-2 1007 ¶4)

Chilichonse chimene chinkagwiritsidwa ntchito pa kulambira konyenga chinkafunika kuwonongedwa (De 12:​2, 3)

Aliyense ankafunika kumalambira Yehova pamalo amene Yehovayo anasankha (De 12:​11-​14; it-1 84 ¶3)

Yehova amafuna kuti anthu ake azimulambira ndi moyo wawo wonse, azikana kulambira konyenga komanso azikhala ogwirizana.

Anthu akulambira Yehova m’njira imene imamusangalatsa. 1. Mlongo wachikulire akulalikira kwa munthu amene amamusamalira. 2. Bambo akuwotcha zinthu zimene ankazigwiritsa ntchito pochita zamizimu. 3. Alongo atatu osiyana mitundu ali pamsonkhano wamayiko.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena