Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsamba 9
  • Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Agibeoni

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Agibeoni
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Agibeoni Anzeru
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Yoswa ndi anthu a ku Gibiyoni
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mawu Omaliza Amene Yoswa Analimbikitsa Nawo Mtundu wa Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 September tsamba 9
Zithunzi zosonyeza ntchito zosiyanasiyana zimene Agibeoni anapatsidwa. 1. Mwamuna wanyamula mtolo wa nkhuni. 2. Mwamuna akumanga mtolo wa nkhuni. 3. Mwamuna wanyamula mitsuko ya madzi pogwiritsa ntchito thabwa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Agibeoni

Agibeoni anachita zinthu mwanzeru (Yos 9:3-6; it-1 930-931)

Akulu a ku Isiraeli anachita zinthu mopanda nzeru chifukwa sanafunsire malangizo kwa Yehova (Yos 9:14, 15; w11 11/15 8 ¶14)

Agibeoni ankatumikira Aisiraeli modzichepetsa (Yos 9:25-27; w04 10/15 18 ¶14)

Agibeoni anadzichepetsa n’kumagwira ntchito zonyozeka chifukwa ankafuna kuti Yehova aziwakonda. Kodi ifeyo tingatani kuti tizichita zinthu modzichepetsa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena