Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 4
  • Zimene Tingaphunzire pa Kusamvana kwa Mafuko a Aisiraeli

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tingaphunzire pa Kusamvana kwa Mafuko a Aisiraeli
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Mawu Omaliza Amene Yoswa Analimbikitsa Nawo Mtundu wa Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Okhutira Komanso Odzichepetsa?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yehova Anamenyera Nkhondo Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 4
Aisiraeli omwe ankakhala kum’mawa kwa Yorodano akuyankha Aisiraeli anzawo omwe ankawaganizira kuti ndi olakwa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzire pa Kusamvana kwa Mafuko a Aisiraeli

Mafuko amene ankakhala kum’mawa kwa Yorodano anamanga guwa lansembe lalikulu komanso lochititsa chidwi (Yos 22:10)

Mafuko enawo anawaimba mlandu kuti achita zosakhulupirika (Yos 22:12, 15, 16; w06 4/15 5 ¶3)

Mafuko amene ankaganiziridwa kuti ndi olakwawo anayankha mofatsa ndipo zimenezi zinathandiza kuti pasakhale nkhondo (Yos 22:21-30; w08 11/15 18 ¶5)

Kodi nkhani imeneyi ikutiphunzitsa chiyani pa zimene tingachite ngati ena akutiganizira zolakwika komanso kufunika komvetsa nkhani yonse tisanaweruze anthu ena?​—Miy 15:1; 18:13.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena