Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 6
  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Okhutira Komanso Odzichepetsa?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Okhutira Komanso Odzichepetsa?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mungatani Kuti Yehova Azikudalitsani?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • “Nthawi Yomweyo Ndinapemphera”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Baibulo Ndi Buku Limene Limanena Zoona
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Okhutira Komanso Odzichepetsa?

Mneneri wa Mulungu anakana kulandira mphatso zapamwamba za Yerobowamu (1Mf 13:7-10; w08 8/15 8 ¶4)

Pambuyo pake mneneriyo anaphwanya lamulo lachindunji la Yehova (1Mf 13:14-19; w08 8/15 11 ¶15)

Kusamvera kwa mneneriyu kunamubweretsera mavuto (1Mf 13:20-22; w08 8/15 9 ¶10)

Makolo akukambirana zokhudza ndalama ndipo ana awo akusewera cha patali.

Tikakhala okhutira n’kumadalira Yehova posankha zochita, tikhoza kupewa mavuto ambiri.​—1Ti 6:8-10

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndine wokhutira ndi zinthu zofunika zimene ndili nazo? Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndine wodzichepetsa ndikamasankha zochita?’​—Miy 3:5; 11:2.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena