Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 6
  • “Nthawi Yomweyo Ndinapemphera”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Nthawi Yomweyo Ndinapemphera”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Pitirizani Kugonjetsa Choipa mwa Kuchita Chabwino”
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • “Inu Mulungu Wanga, Mundikumbukire pa Zabwino Zimene Ndinachita”
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Mfundo Zazikulu za M’buku la Nehemiya
    Nsanja ya Olonda—2006
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Nthawi Yomweyo Ndinapemphera”

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Nehemiya.]

Nehemiya anapemphera asanayankhe funso la mfumu (Ne 2:2-4; w08 2/15 3 ¶5)

Mfumu inachita zimene Nehemiya anapempha (Ne 2:5, 6)

Wachinyamata yemwe ndi wa Mboni akufotokoza zimene amakhulupirira kwa aphunzitsi ake m’kalasi. M’kalasimo akongoletsamo ndi mitundu ya utawaleza pofuna kulimbikitsa ufulu wa amuna amene amagona ndi amuna anzawo.

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi tingatani ngati, tisanakonzekere, tafunsidwa kuti tifotokoze zimene timakhulupirira?​—be 177 ¶4.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena