July Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, July-August 2023 July 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Musakalowerere Ntchito Yomanga” MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Kuteteza . . . ndi Kukhazikitsa Mwalamulo Ntchito ya Uthenga Wabwino” July 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zochita za Ezara Zinachititsa Kuti Dzina la Yehova Lilemekezedwe July 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kusamvera Kumapweteketsa July 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Nthawi Yomweyo Ndinapemphera” July 31–August 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mumagwira Ntchito Zonyozeka? August 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Amachita Khama Kuti Atitumikire August 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo” MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zochita Zanu Zingathandize Banja Lanu Kukhala Losangalala August 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Muli ndi Zolinga Zotani M’chaka Chautumiki Chikubwerachi? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Ntchito Yapadera Yolengeza za Ufumu wa Mulungu mu September August 28–September 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzikhala Okhulupirika kwa Yehova Mukamasankha Anthu Ocheza Nawo MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tsanzirani Chikondi Chokhulupirika cha Yehova KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene