Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 8
  • Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Pitirizani Kugonjetsa Choipa mwa Kuchita Chabwino”
    Nsanja ya Olonda—2007
  • “Inu Mulungu Wanga, Mundikumbukire pa Zabwino Zimene Ndinachita”
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Mfundo Zazikulu za M’buku la Nehemiya
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Malinga a Yerusalemu
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 8
Nehemiya ndi Aisiraeli ena akugwira limodzi ntchito yomanganso mpanda wa Yerusalemu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Nehemiya Ankafuna Kutumikira, Osati Kutumikiridwa

Nehemiya sanagwiritse ntchito udindo wake kuti adzipindulitse yekha (Ne 5:14, 15, 17, 18; w02 11/1 27 ¶3)

Sikuti Nehemiya ankangoyang’anira, koma ankagwiranso nawo ntchitoyo (Ne 5:16; w16.09 6 ¶16)

Nehemiya anapempha Yehova kuti amukumbukire chifukwa cha kudzipereka komanso chikondi chimene anasonyeza (Ne 5:19; w00 2/1 32)

Ngakhale kuti Nehemiya anali bwanamkubwa, sankayembekezera kuti azilandira ulemu wapadera. Iye ndi chitsanzo chabwino kwa anthu amene ali ndi mwayi wa utumiki wapadera komanso maudindo mu mpingo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimakhala wofunitsitsa kuchitira ena zinthu, kapena ndimangofuna kuti anthu azindichitira ineyo zinazake?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena