CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Baibulo Ndi Buku Limene Limanena Zoona
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Mbiri.]
Adamu anali munthu weniweni (1Mb 1:1; w09 9/1 14 ¶1)
Nayenso Nowa anali munthu weniweni (1Mb 1:4; w08 6/1 3 ¶4)
Tikamvetsa kuti anthu otchulidwa m’Baibulo sanali ongopeka koma anthu enieni, zimakhala zosavuta kuti tiziphunzirapo kanthu pa zitsanzo zawo.—1Ak 15:22; w09 9/1 14-15.