January Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu, January-February 2023 January 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino? January 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto January 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Baibulo Ndi Buku Limene Limanena Zoona MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzikhulupirira Kwambiri Mawu a Mulungu January 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mapemphero Anga Amasonyeza Kuti Ndine Wotani? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzikonzekereratu Panopa Zimene Mudzachite Mukadzadwala January 30–February 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Angakuthandizeni Kuti Mukwanitse Kuchita Utumiki Wovuta MOYO WATHU WACHIKHRISTU Yehova Amatithandiza Tikamakumana ndi Mayesero February 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzidziwa Mmene Yehova Amaganizira MOYO WATHU WACHIKHRISTU Khalani ndi Zolinga pa Nyengo ya Chikumbutso February 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zinthu Zimatiyendera Bwino Tikamatsatira Malangizo February 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzikhalabe Wosangalala Ngakhale Pamene Zinthu Sizikuyenda Bwino February 27–March 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzigwiritsa Ntchito Mfundo za M’Baibulo Pothandiza Ana Anu Kuti Zinthu Ziwayendere Bwino KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Zimene Tinganene