Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 8
  • Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • “Usadzachite Nawo Mgwirizano wa Ukwati”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Chitsanzo Chabwino cha Kuphunzitsa Ena
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • “Ine Ndinauka Monga Mayi mu Isiraeli”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Akazi Awiri Olimba Mtima
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 8
Mneneri wamkazi Debora wakhala pansi pa mtengo wa kanjedza, ndipo akulimbikitsa Baraki kuti akathandize anthu a Mulungu.

Debora akulimbikitsa Baraki kuti athandize anthu a Mulungu

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake

Mdani woopsa anapondereza Aisiraeli (Owe 4:3; 5:6-8; w15 8/1 13 ¶1)

Yehova anasankha Debora kuti apulumutse anthu ake (Owe 4:4-7; 5:7; w15 8/1 13 ¶2; onani chithunzi chapachikuto)

Yehova anagwiritsa ntchito Yaeli kuti aphe Sisera (Owe 4:16, 17, 21; w15 8/1 15 ¶1)

Zithunzi: 1. Mneneri wamkazi Debora wakhala pansi pa mtengo wa kanjedza, ndipo akulimbikitsa Baraki kuti akathandize anthu a Mulungu. 2. Yaeli watenga chikhomo cha hema ndi hamala ndipo ali pafupi ndi Sisera amene wagona tulo tofa nato.

Kodi nkhaniyi ikusonyeza kuti Yehova amawaona bwanji akazi?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena