Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 11
  • Muzidziletsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzidziletsa
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Zomwe Ndiyenera Kudziwa pa Nkhani Yosuta Kapena Kuvepa
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • Kodi Ndiyenera Kudziwa Chiyani Zokhudza Kusuta Fodya?
    Galamukani!—2011
  • Kodi Ndingachikanize Motani Chitsenderezo cha Kusuta?
    Galamukani!—1991
  • Kodi Mawu a Mulungu Amati Chiyani pa Nkhani ya Kusuta Fodya?
    Nsanja ya Olonda—2014
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 11

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzidziletsa

Monga anthu opanda ungwiro, nthawi zina zimativuta kuti tizilamulira zomwe timalakalaka. Titamangochita zilizonse zomwe tikufuna, Yehova sangamasangalale nafe. Mwachitsanzo, anthu ena amakonda kwambiri zakudya, zovala komanso malo okhala kuposa mmene amakondera Mulungu. Enanso amakhutiritsa zilakolako zawo zakugonana m’njira imene imaphwanya mfundo za Mulungu. (Aro 1:26, 27) Pamene enanso amangotengera zochita za anzawo n’cholinga choti aziwakonda komanso asaoneke otsalira.​—Eks 23:2.

Kodi tingatani kuti tizilamulira zimene timalakalaka? Tikuyenera kuchita zonse zimene tingathe kuti tiziona kuti ubwenzi wathu ndi Yehova ndi umene uli wofunika kwambiri. (Mt 4:4) Tiyeneranso kupempha Yehova kuti atithandize kukhala odziletsa. Chifukwa chiyani? Chifukwa amadziwa zimene zili zabwino kwa ife komanso mmene angakhutiritsire zolakalaka zathu zoyenera.​—Sl 145:16.

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUSAWONONGE MOYO WANU CHIFUKWA CHA KUSUTA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Chithunzi cha mu vidiyo yakuti “Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta.” Mapapo a munthu amene amasuta akukhosomola kwambiri.

    N’chifukwa chiyani anthu ena amasuta?

  • Chithunzi cha mu vidiyo yakuti “Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta.” Mapapo a munthu amene amasuta akukhosomola kwambiri.

    Kodi kusuta kungakukhudzeni bwanji?

  • Chithunzi cha mu vidiyo yakuti “Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta.” Mapapo a munthu amene amasuta akukhosomola kwambiri.

    N’chifukwa chiyani kusuta komanso kuvepa n’koipa?​—2Ak 7:1

  • Chithunzi cha mu vidiyo yakuti “Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta.” Mapapo a munthu amene amasuta akukhosomola kwambiri.

    Mukhoza kuthana ndi chibaba

    Kodi mungakane bwanji ngati wina atakuuzani kuti musute? Nanga mungathetse bwanji chizolowezi chosuta?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena