KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Zimene Tinganene
Ntchito Yapadera Yoyambitsa Maphunziro a Baibulo (September 1-30)
Funso: Kodi n’zotheka kukhala ndi moyo mpaka kalekale?
Lemba: Sl 37:29
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingakhulupiriredi zimene Baibulo limalonjeza?
Ulendo Woyamba
Funso: Kodi tingapeze kuti malangizo othandiza masiku ano?
Lemba: 2Ti 3:16, 17
Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani tiyenera kudalira Baibulo?
Ulendo Wobwereza
Funso: N’chifukwa chiyani tiyenera kudalira Baibulo?
Lemba: Yob 26:7
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Baibulo linalosera zotani zokhudza masiku athu ano?