Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 8
  • Kuchita Zinthu Ndi Mtima Wonse Kumabweretsa Madalitso Ambiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuchita Zinthu Ndi Mtima Wonse Kumabweretsa Madalitso Ambiri
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yoasi Anasiya Kutumikira Yehova Chifukwa Chocheza ndi Anthu Ochita Zoipa
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Zimene Adani Athu Amachita Pofuna Kutifooketsa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • “Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 8
Elisa akupereka malangizo kwa Mfumu Yehoasi ali pabedi lake pamene akudwala. Yehoasi wanyamula mivi 4.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kuchita Zinthu Ndi Mtima Wonse Kumabweretsa Madalitso Ambiri

Elisa anauza Mfumu Yehoasi kuti ichite zinthu zoyerekezera zosonyeza mmene Aisiraeli adzagonjetsere Asiriya (2Mf 13:15-18)

Yehoasi sanachite zinthu ndi mtima wonse ndipo zimenezi zinachititsa kuti asapambane nkhondo zonse (2Mf 13:19; w10 4/15 26 ¶11)

Yehova amadalitsa kwambiri atumiki ake amene amamufunafuna ndi mtima wonse (Ahe 11:6; w13 11/1 11 ¶5-6)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimasonyeza bwanji kuti ndimachita zinthu ndi mtima wonse pa zinthu zokhudza kulambira monga kuwerenga Baibulo, kupezeka pamisonkhano komanso ntchito yolalikira?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena