Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 9
  • Yehova Sangaiwale Khama Limene Tinachita Pomutumikira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Sangaiwale Khama Limene Tinachita Pomutumikira
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Sangaiwale Chikondi Chanu
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Muzikumbukira Atumiki a Nthawi Zonse
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Kodi Mungatani Kuti Muzisangalala Ndi Ntchito Yanu?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Mungaphunzire Zambiri Kuchokera kwa Achikulire
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 9
Zithunzi za muvidiyo yakuti “Yehova Saiwala.” 1. Chithunzi choyerekezera M’bale David Hibshman ndi Aubrey Bivens atanyamula zikwangwani ku Kentucky street. Zikwangwanizo zimaitanira nkhani yakuti “Dziwani Zoona” yomwe inakambidwa ndi M’bale Joseph Rutherford. 2. M’bale Hibshman ali pamsonkhano ndi abale anzake a mu Komiti ya Nthambi ku Guatemala. 3. M’bale Hibshman akujambulitsa chithunzi ndi abale ndi alongo kumsonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Yehova Sangaiwale Khama Limene Tinachita Pomutumikira

Nthawi zina tikhoza kumva mumtima mwathu kuti anthu sanayamikire komanso aiwala mwamsanga ntchito imene tagwira mwakhama pothandiza ena. Koma nanga bwanji ntchito imene timagwirira Yehova? Mulungu wathu woyamikira Yehova, saiwala zinthu zonse zimene tinachita mwakhama pomutumikira. Ngakhale titakhala kuti sitikuchita zambiri chifukwa cha mavuto a thanzi lathu, iye sadzatisiya.​—Ahe 6:10.

ONERANI VIDIYO YAKUTI YEHOVA SAIWALA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi M’bale Hibshman anasonyeza bwanji kuti anatumikira Yehova mwakhama m’ma utumiki osiyanasiyana?

  • Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti sanaiwale m’baleyu mkazi wake atamwalira, komanso pamene sankachita zambiri chifukwa cha ukalamba?

  • N’chifukwa chiyani tinganene kuti m’baleyu wapeza madalitso ambiri pa zaka zonse zimene wakhala akuchita utumiki wa nthawi zonse?​—Miy 10:22

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena