Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 15
  • Mapemphero Athu ndi Amtengo Wapatali kwa Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mapemphero Athu ndi Amtengo Wapatali kwa Yehova
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Pemphero Lingakuthandizeni Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu
    Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?
  • Kodi Mapemphero Anu ‘Amakonzedwa Ngati Chofukiza’?
    Nsanja ya Olonda—1999
  • Mapemphero Amene Amayankhidwa
    Nsanja ya Olonda—1988
  • Kodi Mapemphero Anu Ali a Tanthauzo Motani?
    Nsanja ya Olonda—1987
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 15
Zithunzi zosonyeza abale ndi alongo akupemphera m’mayiko osiyanasiyana: 1. Kamtsikana pa nthawi yogona ndipo mayi ake ali pafupi naye. 2. Mwamuna ali ndi mkazi wake amene akudwala. 3. M’bale akukwera phiri. 4. Mlongo amene ali ndi nkhawa. 5. Mlongo asanayambe kuphunzira. 6. M’bale yemwe ali m’dziko losauka. 7. Makolo ndi mwana wawo wamkazi asanayambe kudya.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mapemphero Athu ndi Amtengo Wapatali kwa Yehova

Mapemphero ovomerezeka ali ngati zofukiza zonunkhira zomwe zinkafukizidwa nthawi ndi nthawi pamaso pa Yehova ku kachisi. (Sl 141:2) Tikamauza Atate wathu akumwamba m’pemphero kuti timawakonda komanso kuwayamikira, kuwauza zimene zikutidetsa nkhawa komanso zimene tikufuna ndiponso kuwapempha kuti azititsogolera, timasonyeza kuti timaona kuti ubwenzi wathu ndi iwowo ndi wamtengo wapatali. Yehova amaona kuti mapemphero apagulu achidule amene amaperekedwa pa misonkhano yathu ndi mbali yofunika pa kulambira kwathu. Komabe, Yehova ayenera kuti amasangalala kwambiri ngati, pamene tikupemphera patokha, timamuuza zonse za mumtima mwathu komanso kwa kanthawi ndithu.​—Miy 15:8.

ONERANI VIDIYO YAKUTI NDIMAKONDA KUPEMPHERA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi M’bale Johnson wachita ma utumiki osiyanasiyana ati m’gulu la Yehova?

  • Kodi pemphero linathandiza bwanji M’bale Johnson kudalira Yehova?

  • Kodi mwaphunzira chiyani kuchokera pa zimene zinachitikira m’baleyu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena