Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 7
  • “Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe”​—2Mf 9:8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe”​—2Mf 9:8
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Anapereka Chilango kwa Mfumukazi Yoipa
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • A6-A Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 1)
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yezebeli—Mkazi Woipa wa Mfumu
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu
    Nkhani Zina
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA MMAWU A MULUNGU

“NYUMBA YONSE YA AHABU IFAFANIZIDWE”​—2Mf 9:8

“Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe.” Tchati chosonyeza zochitika za m’nyumba ya Ahabu.

UFUMU WA YUDA

Yehosafati anakhala mfumu

c. 911 B.C.E: Yehoramu (mwana wa Yehosafati; mwamuna wa Ataliya, mwana wamkazi wa Ahabu ndi Yezebeli) anayamba kulamulira yekha

c. 906 B.C.E: Ahaziya (mdzukulu wa Ahabu ndi Yezebeli) anakhala mfumu

c. 905 B.C.E: Ataliya anapha ana onse a m’banja la chifumu ndipo anayamba kulamulira. Mdzukulu wake mmodzi yekha Yehoasi ndi amene anapulumuka ndipo anabisidwabe kwa kanthawi ndi Mkulu wa Ansembe Yehoyada.​—2Mf 11:1-3

898 B.C.E: Yehoasi anakhala mfumu. Mfumukazi Ataliya inaphedwa ndi Mkulu wa Ansembe Yehoyada.​—2Mf 11:4-16

UFUMU WA ISIRAELI

c. 920 B.C.E: Ahaziya (mwana wa Ahabu ndi Yezebeli) anakhala mfumu

c. 917 B.C.E: Yehoramu (mwana wa Ahabu ndi Yezebeli) anakhala mfumu

c. 905 B.C.E: Yehu anapha Mfumu Yehoramu ya Isiraeli ndi azichimwene ake, mayi ake a Yehoramu (Yezebeli) komanso Mfumu Ahaziya ya ku Yuda ndi azichimwene ake.​—2Mf 9:14–10:17

c. 904 B.C.E: Yehu anayamba kulamulira monga mfumu

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena