Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 6
  • N’chifukwa Chiyani Akhristu Akufunika Kuyesetsa Kuti Akhale Ndi Zolinga?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • N’chifukwa Chiyani Akhristu Akufunika Kuyesetsa Kuti Akhale Ndi Zolinga?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Alongo Angatani Kuti Azichita Zambiri Potumikira Yehova?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mmene Mungakwaniritsire Zolinga Zanu Zauzimu
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2006
  • “Mwamuna Wake Amadziwika Pazipata”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo​—Chikhulupiriro
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 6

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

N’chifukwa Chiyani Akhristu Akufunika Kuyesetsa Kuti Akhale Ndi Zolinga?

Abale ndi alongo amayesetsa kuti akhale ndi zolinga zauzimu monga kuchita upainiya, kutumikira pa Beteli komanso kugwira nawo ntchito yomanga ndi kukonza Nyumba za Ufumu. Kuwonjezera pamenepo, abale amayesetsa kuti akhale oyang’anira. (1Ti 3:1) Koma kodi zimenezi zikutanthauza kuti Akhristu akuyenera kuyesetsa kukhala ndi zolinga n’cholinga chofuna kutchuka kapena kuoneka kukhala ofunika kuposa ena?

ONERANI VIDIYO YAKUTI N’CHIFUKWA CHIYANI MUKUFUNIKA KUYESETSA KUTI MUKHALE WOYANG’ANIRA? (1TI 3:1), KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

Kodi malemba otsatirawa angatithandize bwanji kudziwa zifukwa zitatu zimene zingatichititse kuyesetsa kukhala ndi zolinga?

  • Mt 5:14-16

  • 1Ti 4:15

  • Ahe 5:14–6:1

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena