Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 6
  • Kodi Mapemphero Anga Amasonyeza Kuti Ndine Wotani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mapemphero Anga Amasonyeza Kuti Ndine Wotani?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Wakumva Pemphero”
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Mapemphero Amene Amayankhidwa
    Nsanja ya Olonda—1988
  • Kodi Ndimapemphero Ayani Omwe Amayankhidwa?
    Nsanja ya Olonda—1991
  • Pemphero Lingakuthandizeni Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu
    Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mapemphero Anga Amasonyeza Kuti Ndine Wotani?

Yabezi anali wolemekezeka kwambiri (1Mb 4:9)

Pemphero lake linasonyeza kuti ankaganizira kwambiri kulambira koona (1Mb 4:10a; w10 10/1 23 ¶3-7)

Yehova anayankha pemphero la Yabezi (1Mb 4:10b)

Mlongo wachikulire akupemphera mochokera pansi pa mtima. Ndipo ali ndi Baibulo komanso pepala lomwe pali mayina abale ndi alongo omwe ali m’ndende.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi mapemphero anga amasonyeza kuti ndine wotani?’​—Mt 6:9, 10.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena